100.The Chargers

  1. Palizothamangakwambirindikupumakwawokofulumira
  2. Ndi zimene zimaonetsa moto zikamathamanga
  3. Ndipo zimachita nkhondo m’mbandakucha
  4. Ndi kuonetsa fumbi
  5. Ndi kuphwanya pakati gulu la adani
  6. Ndithudi! Munthu sathokoza kwaAmbuye wake
  7. Ndipo mwini wake amachitira umboni zimenezi
  8. Ndithudi iye ali kukonda chuma kwambiri
  9. Kodi iye sadziwa kuti pamene zonse zili m’manda zidzatulutsidwa ndi kuonetsedwa poyera
  10. Ndizonsezimenezilim’mitimayaanthuzizidzaululidwa
  11. Ndithudi, patsiku limeneli, Ambuye wako adzakhala ali kudziwa chilichonse