103.The Declining Day, Epoch

  1. Pali nthawi
  2. Ndithudi ! Munthu ndi otayika
  3. Kupatula okhawo amene amakhulupirira ndi kuchita ntchito zabwino ndipo amalimbikitsana wina ndi mzake kuchita chilungamo ndi kukumbutsana kupirira