105.The Elephant

  1. Kodi siudaone mmene Mulungu adachitira ndi eni ake a Njovu
  2. Kodi Iye sadasokoneze chiwembu chawo
  3. Ndipo anatumiza gulu la mbalame lolimbana nawo
  4. Zimene zinawalasa miyala ya moto
  5. Ndipo iwo adaoneka ngati msipu wodyedwa