106.Quraysh

  1. Pofuna kuteteza mtundu wa Quraish
  2. Kuti apitirire pa maulendo nthawi ya Chilimwe ndi m’nthawi ya Chisanu
  3. Motero auzeni kuti azipembedza Ambuye wa Nyumba ino
  4. Amene wawadyetsa m’masiku a njala ndi kuwachotsa mantha