109.The Disbelievers

  1. Nena: oh! Inu anthu osakhulupirira
  2. Ine sindipembedza chimene inu mupembedza
  3. Ndiponso inu simudzapembedza chimene ine ndipembedza
  4. Ndipo ine sindidzapembedza chimene inu muli kuchipembedza
  5. Ndipo inu simudzapembedza chimene ine ndimapembedza
  6. Kwa inu chipembedzo chanu ndipo kwa ine chipembedzo changa