110.Divine Support

  1. Pamene chithandizo cha Mulungu chidza ndi kupambana
  2. Ndipo uona anthu akulowa m’chipembedzo cha Mulungu mu unyinji wawo
  3. Motero lemekeza Ambuye wako ndipo upemphe chikhululukiro chake. Ndithudi Iye amavomera kulapa ndipo ndi wokhululukira