111.The Palm Fibre

  1. Aonongeke manja a Abu Lahab, ndipo nayenso aonongeke
  2. Chuma chake ndi ana ake sizidzamuthandiza ai
  3. Iye adzalowa m’moto wa lawilawi
  4. Ndipo mkazi wake amene amanyamula nkhuni
  5. Mkhosi mwake muli chingwe chopota cha mlaza