113.The Dawn

  1. Nena: “Ine ndifuna kuthawira kwa Ambuye wa M’mbandakucha
  2. Kuchokera ku zinthu zonyansa zimene walenga
  3. Ndi kuchokera ku zonyansa za nthawi ya usiku pamene mdima ufika
  4. Ndi kuchokera ku zonyansa za anthu a matsenga pamene auzila pfundo
  5. “Ndi ku zonyansa za munthu wa dumbo pamene achita nsanje.”