114.Mankind

  1. Nena: “Ine ndifuna kuthawira kwa Ambuye wa anthu
  2. Mfumu ya anthu
  3. Mulungu wa anthu
  4. Kuchokera ku zonyansa za kazitape amene amachoka akatha
  5. Amene amanong’oneza m’mitima mwa anthu
  6. Ya majini ndi anthu.”